-
Ezekieli 25:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Pa chifukwa chimenechi, ndikuperekani kwa anthu a Kumʼmawa kuti mukhale chuma chawo. Iwo adzamanga misasa yokhala ndi mipanda komanso adzakhoma matenti awo mʼdziko lanu. Adzadya zokolola zanu ndipo adzamwa mkaka wa ziweto zanu.
-