Ezekieli 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Chifukwa chakuti munawomba mʼmanja+ ndi kuponda pansi mwamphamvu, komanso munasangalala monyoza poona zimene zinachitikira dziko la Isiraeli,+
6 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Chifukwa chakuti munawomba mʼmanja+ ndi kuponda pansi mwamphamvu, komanso munasangalala monyoza poona zimene zinachitikira dziko la Isiraeli,+