-
Ezekieli 25:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Anthu amenewa ndidzawachitira zinthu zopweteka powabwezera ndipo ndidzawalanga mwaukali. Ndikadzawalanga, adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”
-