Ezekieli 26:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, Turo wanena Yerusalemu+ kuti, ‘Eyaa! Zakhala bwino. Mzinda umene unkakopa anthu a mitundu ina wathyoledwa.+ Tsopano zinthu zindiyendera bwino ndipo ndilemera chifukwa mzindawo wawonongedwa.’
2 “Iwe mwana wa munthu, Turo wanena Yerusalemu+ kuti, ‘Eyaa! Zakhala bwino. Mzinda umene unkakopa anthu a mitundu ina wathyoledwa.+ Tsopano zinthu zindiyendera bwino ndipo ndilemera chifukwa mzindawo wawonongedwa.’