Ezekieli 26:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ziboda za mahatchi ake zidzapondaponda mʼmisewu yako yonse.+ Iye adzapha anthu ako ndi lupanga ndipo zipilala zako zikuluzikulu zidzagwa.
11 Ziboda za mahatchi ake zidzapondaponda mʼmisewu yako yonse.+ Iye adzapha anthu ako ndi lupanga ndipo zipilala zako zikuluzikulu zidzagwa.