Ezekieli 26:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Akalonga* onse akunyanja adzatsika mʼmipando yawo yachifumu nʼkuvula mikanjo yawo* komanso zovala zawo za nsalu yopeta. Iwo azidzanjenjemera chifukwa cha mantha. Adzakhala padothi ndipo nthawi zonse azidzanjenjemera nʼkumakuyangʼanitsitsa modabwa.+
16 Akalonga* onse akunyanja adzatsika mʼmipando yawo yachifumu nʼkuvula mikanjo yawo* komanso zovala zawo za nsalu yopeta. Iwo azidzanjenjemera chifukwa cha mantha. Adzakhala padothi ndipo nthawi zonse azidzanjenjemera nʼkumakuyangʼanitsitsa modabwa.+