-
Ezekieli 26:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 ndidzakutsitsira mʼdzenje* limodzi ndi anthu enanso amene akutsikira mʼmanda momwe muli anthu amene anafa kalekale. Ndidzakuchititsa kuti ukhale mʼmalo otsika kwambiri mofanana ndi malo ena akalekale amene anawonongedwa. Udzakhala kumeneko pamodzi ndi ena onse amene akutsikira kumanda+ kuti anthu asadzakhalenso mwa iwe. Kenako ndidzalemekeza* dziko la anthu amoyo.
-