Ezekieli 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndidzakugwetsera zoopsa modzidzimutsa ndipo sudzakhalaponso.+ Anthu adzakufunafuna koma sudzapezeka mpaka kalekale,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
21 Ndidzakugwetsera zoopsa modzidzimutsa ndipo sudzakhalaponso.+ Anthu adzakufunafuna koma sudzapezeka mpaka kalekale,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”