Ezekieli 27:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anakupanga ndi matabwa a mtengo wa junipa* ochokera ku Seniri,+Ndipo anatenga mkungudza wa ku Lebanoni kuti ukhale mtengo wako womangirirapo chinsalu choyendetsera ngalawa.
5 Anakupanga ndi matabwa a mtengo wa junipa* ochokera ku Seniri,+Ndipo anatenga mkungudza wa ku Lebanoni kuti ukhale mtengo wako womangirirapo chinsalu choyendetsera ngalawa.