Ezekieli 27:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Amuna odziwa ntchito* komanso aluso a ku Gebala+ ndi amene ankamata molumikizira matabwa ako.+ Sitima zonse zapanyanja ndi anthu amene ankaziyendetsa ankabwera kwa iwe kudzagulitsa malonda.
9 Amuna odziwa ntchito* komanso aluso a ku Gebala+ ndi amene ankamata molumikizira matabwa ako.+ Sitima zonse zapanyanja ndi anthu amene ankaziyendetsa ankabwera kwa iwe kudzagulitsa malonda.