-
Ezekieli 27:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Amuna a ku Arivadi amene ali mʼgulu la asilikali ako anaima pamwamba pa mpanda wako kuzungulira mzinda wonse,
Ndipo amuna olimba mtima ankalondera nsanja zako.
Iwo anapachika zishango zawo zozungulira mʼmakoma kuzungulira mpanda wako wonse,
Ndipo anachititsa kuti ukhale wokongola kwambiri.
-