Ezekieli 27:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yuda komanso dziko la Isiraeli linachita nawe malonda. Anakupatsa tirigu wa ku Miniti,+ zakudya zapamwamba, uchi,+ mafuta ndi basamu+ posinthanitsa ndi katundu wako.+
17 Yuda komanso dziko la Isiraeli linachita nawe malonda. Anakupatsa tirigu wa ku Miniti,+ zakudya zapamwamba, uchi,+ mafuta ndi basamu+ posinthanitsa ndi katundu wako.+