-
Ezekieli 27:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Mʼmisika yako iwo ankachita malonda a zovala zokongola kwambiri, malaya opangidwa ndi nsalu yabuluu komanso nsalu yopeta yamitundu yosiyanasiyana ndi makapeti okhala ndi mitundu yosiyanasiyana. Zinthu zonsezi ankazimanga bwinobwino ndi zingwe.
-