Ezekieli 27:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Sitima zapamadzi za ku Tarisi+ zinkanyamula katundu wako wamalonda,Choncho unali ndi chuma chambiri ndipo unalemera* pakati pa nyanja.
25 Sitima zapamadzi za ku Tarisi+ zinkanyamula katundu wako wamalonda,Choncho unali ndi chuma chambiri ndipo unalemera* pakati pa nyanja.