-
Ezekieli 27:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 Anthu onse opalasa ngalawa, oyendetsa sitima zapamadzi komanso anthu onse amene amagwira ntchito mʼsitima zapamadzi
Adzatsika mʼsitima zawo nʼkukaima pamtunda.
-