Ezekieli 27:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Amalonda ochokera pakati pa mitundu ina ya anthu adzakuimbira mluzu chifukwa cha zimene zakuchitikira. Mapeto ako adzafika modzidzimutsa ndipo adzakhala owopsa,Moti sudzakhalaponso mpaka kalekale.’”’”+
36 Amalonda ochokera pakati pa mitundu ina ya anthu adzakuimbira mluzu chifukwa cha zimene zakuchitikira. Mapeto ako adzafika modzidzimutsa ndipo adzakhala owopsa,Moti sudzakhalaponso mpaka kalekale.’”’”+