-
Ezekieli 28:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kodi amene adzakuphe udzamuuzabe kuti, ‘Ine ndine mulungu?’
Kwa anthu amene adzakuipitse, iwe udzakhala munthu wamba, osati mulungu.”’
-