Ezekieli 28:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iwe unali mu Edeni, munda wa Mulungu. Unakongoletsedwa ndi miyala yamtengo wapatali yamitundu yonseMonga rube, topazi, yasipi, kulusolito, onekisi, yade, safiro, nofeki+ ndi emarodi.Zoikamo miyala imeneyi zinali zagolide. Ndinazipanga pa tsiku limene ndinakulenga.
13 Iwe unali mu Edeni, munda wa Mulungu. Unakongoletsedwa ndi miyala yamtengo wapatali yamitundu yonseMonga rube, topazi, yasipi, kulusolito, onekisi, yade, safiro, nofeki+ ndi emarodi.Zoikamo miyala imeneyi zinali zagolide. Ndinazipanga pa tsiku limene ndinakulenga.