-
Ezekieli 29:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Koma ine ndidzakukola ndi ngowe munsagwada zako nʼkuchititsa kuti nsomba zamʼngalande za mtsinje wa Nailo zikakamire kumamba ako.
Ndidzakutulutsa mumtsinje wako wa Nailo pamodzi ndi nsomba zonse zamumtsinje wa Nailo zimene zakakamira kumamba ako.
-