12 Ndidzachititsa kuti dziko la Iguputo likhale lowonongeka kwambiri kuposa mayiko ena onse, ndipo mizinda yake idzakhala yowonongeka kwambiri pa mizinda yonse kwa zaka 40.+ Ndidzamwaza Aiguputo pakati pa anthu a mitundu ina ndipo ndidzawabalalitsira mʼmayiko ena.”+