Ezekieli 29:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Zaka 40 zikadzatha, ndidzasonkhanitsanso Aiguputowo nʼkuwabwezera kudziko lawo kuchokera kwa anthu a mitundu ina kumene anabalalikira.+
13 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Zaka 40 zikadzatha, ndidzasonkhanitsanso Aiguputowo nʼkuwabwezera kudziko lawo kuchokera kwa anthu a mitundu ina kumene anabalalikira.+