Ezekieli 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ufumu wa Iguputo udzakhala wochepa mphamvu kusiyana ndi maufumu ena ndipo sudzalamuliranso mitundu ina ya anthu.+ Ine ndidzawachepetsa kwambiri moti sadzathanso kugonjetsa mitundu ina ya anthu.+
15 Ufumu wa Iguputo udzakhala wochepa mphamvu kusiyana ndi maufumu ena ndipo sudzalamuliranso mitundu ina ya anthu.+ Ine ndidzawachepetsa kwambiri moti sadzathanso kugonjetsa mitundu ina ya anthu.+