Ezekieli 29:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nyumba ya Isiraeli sidzadaliranso ufumu umenewu.+ Koma udzangowakumbutsa zolakwa zimene anachita podalira Aiguputo kuti awathandize. Ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’”
16 Nyumba ya Isiraeli sidzadaliranso ufumu umenewu.+ Koma udzangowakumbutsa zolakwa zimene anachita podalira Aiguputo kuti awathandize. Ndipo adzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”’”