Ezekieli 29:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pa tsiku limenelo, ndidzaphukitsira nyumba ya Isiraeli nyanga*+ ndipo iwe ndidzakupatsa mpata kuti ulankhule pakati pawo, ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”
21 Pa tsiku limenelo, ndidzaphukitsira nyumba ya Isiraeli nyanga*+ ndipo iwe ndidzakupatsa mpata kuti ulankhule pakati pawo, ndipo iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.”