Ezekieli 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsikulo lili pafupi, inde tsiku la Yehova lili pafupi.+ Tsikulo lidzakhala la mitambo+ ndiponso nthawi yoikidwiratu yoti mitundu ya anthu iweruzidwe.+
3 Tsikulo lili pafupi, inde tsiku la Yehova lili pafupi.+ Tsikulo lidzakhala la mitambo+ ndiponso nthawi yoikidwiratu yoti mitundu ya anthu iweruzidwe.+