Ezekieli 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Lupanga lidzabwera kudzaukira Iguputo, ndipo anthu a ku Itiyopiya adzachita mantha kwambiri anthu akadzaphedwa ku Iguputo.Chuma cha Iguputo chidzalandidwa ndipo maziko ake adzagwetsedwa.+
4 Lupanga lidzabwera kudzaukira Iguputo, ndipo anthu a ku Itiyopiya adzachita mantha kwambiri anthu akadzaphedwa ku Iguputo.Chuma cha Iguputo chidzalandidwa ndipo maziko ake adzagwetsedwa.+