-
Ezekieli 30:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 “Iwe mwana wa munthu, ine ndathyola dzanja la Farao mfumu ya Iguputo. Dzanjalo silidzamangidwa kuti lichire kapena kukulungidwa ndi bandeji kuti likhale ndi mphamvu zoti nʼkugwira lupanga.”
-