Ezekieli 30:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ine ndilanga Farao mfumu ya Iguputo+ ndipo ndidzathyola manja ake onse, dzanja lamphamvu ndi lothyoka lomwe.+ Ndidzachititsa kuti lupanga ligwe mʼdzanja lake.+
22 “Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ine ndilanga Farao mfumu ya Iguputo+ ndipo ndidzathyola manja ake onse, dzanja lamphamvu ndi lothyoka lomwe.+ Ndidzachititsa kuti lupanga ligwe mʼdzanja lake.+