Ezekieli 30:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndidzalimbitsa manja a mfumu ya Babulo koma manja a Farao adzafooka. Ndikadzapereka lupanga langa mʼmanja mwa mfumu ya Babulo, iye nʼkuligwiritsa ntchito pomenyana ndi dziko la Iguputo,+ iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.
25 Ndidzalimbitsa manja a mfumu ya Babulo koma manja a Farao adzafooka. Ndikadzapereka lupanga langa mʼmanja mwa mfumu ya Babulo, iye nʼkuligwiritsa ntchito pomenyana ndi dziko la Iguputo,+ iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova.