-
Ezekieli 31:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Mtengowo unakula kwambiri chifukwa cha madzi. Akasupe ozama anachititsa kuti mtengowo utalike.
Pamalo amene mtengowo unadzalidwa panali mitsinje yambiri yamadzi.
Ngalande za madziwo zinkathirira mitengo yonse yamʼmundamo.
-