-
Ezekieli 31:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Nʼchifukwa chake mtengowo unatalika kwambiri kuposa mitengo yonse yamʼmundamo.
Nthambi zake zinachuluka komanso zinatalika
Chifukwa cha kuchuluka kwa madzi mʼmitsinje yake.
-