-
Ezekieli 31:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Mtengowo unakhala wokongola kwambiri ndipo nthambi zake zinatalika kwambiri,
Chifukwa chakuti mizu yake inapita pansi nʼkukafika pamadzi ambiri.
-