Ezekieli 31:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Chifukwa chakuti mtengowu* unatalika kwambiri moti nsonga yake inakafika mʼmitambo, ndipo mtima wake unayamba kudzikuza chifukwa cha kutalika kwake,
10 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Chifukwa chakuti mtengowu* unatalika kwambiri moti nsonga yake inakafika mʼmitambo, ndipo mtima wake unayamba kudzikuza chifukwa cha kutalika kwake,