-
Ezekieli 31:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Zidzakhala choncho kuti pasadzapezekenso mtengo uliwonse umene uli pafupi ndi madzi, womwe udzatalike kwambiri kapena umene nsonga zake zidzafike mʼmitambo. Komanso kuti mtengo uliwonse umene uli pamadzi ambiri usadzatalike kukafika mʼmitambo. Chifukwa mitengo yonse idzafa nʼkutsikira pansi pa nthaka pamodzi ndi ana a anthu amene akutsikira kudzenje.’*
-