-
Ezekieli 31:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Pa tsiku limene mtengowo udzatsikire ku Manda,* ndidzachititsa kuti anthu alire. Choncho ndidzaphimba madzi akuya komanso kutseka mitsinje yake kuti madzi ambiri asamadutse. Ndidzachititsa mdima mu Lebanoni chifukwa cha mtengowo ndipo mitengo yonse yakutchire idzafota.
-