-
Ezekieli 32:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Ndidzanyowetsa dziko ndi magazi amene akutuluka mwamphamvu mʼthupi mwako mpaka kumapiri,
Ndipo adzadzaza mitsinje.
-