Ezekieli 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 ‘Ndidzachititsa kuti mitima ya anthu ambiri ikhale ndi nkhawa ndikadzatenga anthu ako ogwidwa ukapolo nʼkuwapititsa kwa anthu a mitundu ina,Kumayiko amene sukuwadziwa.+
9 ‘Ndidzachititsa kuti mitima ya anthu ambiri ikhale ndi nkhawa ndikadzatenga anthu ako ogwidwa ukapolo nʼkuwapititsa kwa anthu a mitundu ina,Kumayiko amene sukuwadziwa.+