-
Ezekieli 32:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Imeneyi ndi nyimbo yoimba polira ndipo anthu adzaiimba.
Ana aakazi a mitundu ina ya anthu adzaiimba.
Nyimbo imeneyi adzaimbira Iguputo ndi gulu la anthu onse amene amamutsatira,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
-