Ezekieli 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iguputo adzaphedwa pamodzi ndi anthu amene aphedwa ndi lupanga.+ Iye adzaphedwa ndi lupanga. Mukokereni kutali limodzi ndi gulu la anthu ake onse amene amamutsatira.
20 Iguputo adzaphedwa pamodzi ndi anthu amene aphedwa ndi lupanga.+ Iye adzaphedwa ndi lupanga. Mukokereni kutali limodzi ndi gulu la anthu ake onse amene amamutsatira.