Ezekieli 32:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ali pansi pa Manda,* asilikali amphamvu kwambiri adzalankhula ndi iyeyo komanso amene ankamuthandiza. Onsewo adzatsikira kumanda ndipo adzagona limodzi ndi anthu osadulidwa, ataphedwa ndi lupanga.
21 Ali pansi pa Manda,* asilikali amphamvu kwambiri adzalankhula ndi iyeyo komanso amene ankamuthandiza. Onsewo adzatsikira kumanda ndipo adzagona limodzi ndi anthu osadulidwa, ataphedwa ndi lupanga.