-
Ezekieli 32:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 ‘Chifukwa anachititsa kuti anthu amene akukhala mʼdziko la anthu amoyo azikhala mwamantha, Farao ndi gulu lonse la anthu amene ankamutsatira adzaikidwa mʼmanda limodzi ndi anthu osadulidwa. Adzaikidwa mʼmanda pamodzi ndi anthu amene anaphedwa ndi lupanga,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.”
-