-
Ezekieli 33:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Iye anamva kulira kwa lipenga koma sanamvere chenjezolo. Magazi ake adzakhala pamutu pake. Akanamvera chenjezolo, akanapulumutsa moyo wake.
-