-
Ezekieli 33:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndikauza munthu wolungama kuti: “Ndithu, iwe udzapitiriza kukhala ndi moyo,” ndiyeno iyeyo nʼkuyamba kukhulupirira kuti zinthu zolungama zimene anachita mʼmbuyo zidzamupulumutsa nʼkuchita zinthu zoipa,*+ zinthu zonse zolungama zimene anachita zija sizidzakumbukiridwa. Iye adzafa chifukwa cha zinthu zoipa zimene wachita.+
-