Ezekieli 33:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndikauza munthu woipa kuti: “Udzafa ndithu,” ndiyeno iyeyo nʼkusiya machimo akewo, nʼkuyamba kuchita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo,+
14 Ndikauza munthu woipa kuti: “Udzafa ndithu,” ndiyeno iyeyo nʼkusiya machimo akewo, nʼkuyamba kuchita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo,+