Ezekieli 33:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu amene amachita zinthu zabwino akasiya kuchita zabwinozo nʼkumachita zoipa,* akuyenera kufa chifukwa cha zochita zakezo.+
18 Munthu amene amachita zinthu zabwino akasiya kuchita zabwinozo nʼkumachita zoipa,* akuyenera kufa chifukwa cha zochita zakezo.+