Ezekieli 33:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma munthu woipa akasiya kuchita zinthu zoipa nʼkuyamba kuchita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo, adzapitiriza kukhala ndi moyo chifukwa chochita zimenezi.+
19 Koma munthu woipa akasiya kuchita zinthu zoipa nʼkuyamba kuchita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo, adzapitiriza kukhala ndi moyo chifukwa chochita zimenezi.+