Ezekieli 33:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Patapita nthawi, mʼchaka cha 12, mʼmwezi wa 10, tsiku la 5 la mweziwo, kuchokera pamene tinatengedwa kupita ku ukapolo, munthu wina amene anathawa ku Yerusalemu anabwera kwa ine+ nʼkundiuza kuti: “Mzinda uja wawonongedwa!”+
21 Patapita nthawi, mʼchaka cha 12, mʼmwezi wa 10, tsiku la 5 la mweziwo, kuchokera pamene tinatengedwa kupita ku ukapolo, munthu wina amene anathawa ku Yerusalemu anabwera kwa ine+ nʼkundiuza kuti: “Mzinda uja wawonongedwa!”+