Ezekieli 33:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Iwe mwana wa munthu, anthu amene akukhala mʼmabwinjawa+ akulankhula zokhudza dziko la Isiraeli kuti, ‘Abulahamu anali munthu mmodzi, koma anatenga dzikoli kukhala lake.+ Ife tilipo ambiri, choncho dzikoli laperekedwa kwa ife kuti likhale lathu.’
24 “Iwe mwana wa munthu, anthu amene akukhala mʼmabwinjawa+ akulankhula zokhudza dziko la Isiraeli kuti, ‘Abulahamu anali munthu mmodzi, koma anatenga dzikoli kukhala lake.+ Ife tilipo ambiri, choncho dzikoli laperekedwa kwa ife kuti likhale lathu.’