Ezekieli 33:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Inu mukudalira lupanga lanu,+ mukuchita zinthu zonyansa ndipo aliyense wa inu akugona ndi mkazi wa mnzake.+ Ndiye kodi pamenepa ndinu oyenera kutenga dzikoli kuti likhale lanu?”’+
26 Inu mukudalira lupanga lanu,+ mukuchita zinthu zonyansa ndipo aliyense wa inu akugona ndi mkazi wa mnzake.+ Ndiye kodi pamenepa ndinu oyenera kutenga dzikoli kuti likhale lanu?”’+