Ezekieli 33:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma iwe mwana wa munthu, anthu a mtundu wako akukambirana za iwe mʼmbali mwa mpanda komanso mʼmakomo a nyumba.+ Aliyense akuuza mʼbale wake kuti, ‘Bwerani tidzamve mawu ochokera kwa Yehova.’
30 Koma iwe mwana wa munthu, anthu a mtundu wako akukambirana za iwe mʼmbali mwa mpanda komanso mʼmakomo a nyumba.+ Aliyense akuuza mʼbale wake kuti, ‘Bwerani tidzamve mawu ochokera kwa Yehova.’